-
Ezekieli 46:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ngati mtsogoleri wa anthu akupereka kwa ansembe nsembe yopsereza yathunthu+ kapena nsembe zamgwirizano kuti zikhale nsembe yaufulu yoperekedwa kwa Yehova, azimutsegulira geti lakumʼmawa. Mtsogoleriyo azipereka kwa ansembe nsembe yake yopsereza yathunthu ndi nsembe zake zamgwirizano ngati mmene amachitira pa tsiku la Sabata.+ Akatuluka getilo lizitsekedwa.+
-