Ezekieli 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsiku lililonse muzipereka kwa Yehova mwana wa nkhosa wamphongo wopanda chilema wosakwanitsa chaka kuti ikhale nsembe yopsereza yathunthu.+ Muzichita zimenezi mʼmawa uliwonse.
13 Tsiku lililonse muzipereka kwa Yehova mwana wa nkhosa wamphongo wopanda chilema wosakwanitsa chaka kuti ikhale nsembe yopsereza yathunthu.+ Muzichita zimenezi mʼmawa uliwonse.