Ezekieli 46:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako munthu uja anandilowetsa mkati kudzera pakhomo+ limene lili pafupi ndi geti lopita kunyumba zopatulika* zomwe ansembe ankadyeramo, zimene zinayangʼana kumpoto.+ Kumeneko ndinaona malo kumbuyo, mbali yakumadzulo.
19 Kenako munthu uja anandilowetsa mkati kudzera pakhomo+ limene lili pafupi ndi geti lopita kunyumba zopatulika* zomwe ansembe ankadyeramo, zimene zinayangʼana kumpoto.+ Kumeneko ndinaona malo kumbuyo, mbali yakumadzulo.