Ezekieli 46:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼmakona onse 4 a bwalolo munali mabwalo angʼonoangʼono amene anali mikono 40* mulitali ndi mikono 30 mulifupi. Mabwalo 4 onsewo anali aakulu mofanana.*
22 Mʼmakona onse 4 a bwalolo munali mabwalo angʼonoangʼono amene anali mikono 40* mulitali ndi mikono 30 mulifupi. Mabwalo 4 onsewo anali aakulu mofanana.*