-
Ezekieli 46:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Panali kakhoma kuzungulira mkati monse mwa tinyumba tonse 4 tapakonato. Mʼmunsi mwa timakoma timeneto anamangamo malo oti aziwiritsirapo nsembe.
-