Ezekieli 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno ananditulutsa kudzera pageti lakumpoto+ ndipo anandipititsa kunja nʼkuzungulira kukafika kugeti lakunja limene linayangʼana kumʼmawa.+ Kumeneko ndinaonako madzi akuyenda kuchokera kumbali yakumanja kwa getilo.
2 Ndiyeno ananditulutsa kudzera pageti lakumpoto+ ndipo anandipititsa kunja nʼkuzungulira kukafika kugeti lakunja limene linayangʼana kumʼmawa.+ Kumeneko ndinaonako madzi akuyenda kuchokera kumbali yakumanja kwa getilo.