Ezekieli 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu uja anapita mbali yakumʼmawa atatenga chingwe choyezera mʼmanja mwake.+ Kenako anayeza mtsinjewo mikono* 1,000 kuchokera pakanyumba kapageti, ndipo anandiuza kuti ndiwoloke mtsinjewo. Madzi ake anali olekeza mʼmapazi.
3 Munthu uja anapita mbali yakumʼmawa atatenga chingwe choyezera mʼmanja mwake.+ Kenako anayeza mtsinjewo mikono* 1,000 kuchokera pakanyumba kapageti, ndipo anandiuza kuti ndiwoloke mtsinjewo. Madzi ake anali olekeza mʼmapazi.