-
Ezekieli 47:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako anayezanso mtsinjewo mikono ina 1,000 ndipo anandiuza kuti ndiwoloke. Madzi ake anali olekeza mʼmawondo.
Anayezanso mtsinjewo mikono ina 1,000 nʼkundiuza kuti ndiwoloke ndipo madzi ake anali olekeza mʼchiuno.
-