-
Ezekieli 47:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atayezanso mtsinjewo mikono ina 1,000, mtsinjewo unakula kwambiri moti sindinathe kuwoloka chifukwa chakuti madzi ake anali ozama kwambiri moti munthu amafunika kusambira. Unali mtsinje waukulu woti munthu sakanatha kuwoloka.
-