-
Ezekieli 47:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimenezi?”
Kenako munthu uja ananditulutsa mʼmadzimo nʼkupita nane mʼmphepete mwa mtsinjewo.
-