Ezekieli 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Madzi amʼzithaphwi ndi mʼmadambo amʼmphepete mwa nyanjayo sadzasintha nʼkukhala abwino. Madzi amenewo adzakhalabe amchere.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:11 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 113/1/1999, ptsa. 21-22
11 Madzi amʼzithaphwi ndi mʼmadambo amʼmphepete mwa nyanjayo sadzasintha nʼkukhala abwino. Madzi amenewo adzakhalabe amchere.+