Ezekieli 47:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Limeneli ndi dera limene mudzagawire mafuko 12 a Isiraeli ngati cholowa chawo ndipo zigawo ziwiri zidzakhale za mbadwa za Yosefe.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:13 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, ptsa. 17-18, 229/15/1988, ptsa. 25, 27
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Limeneli ndi dera limene mudzagawire mafuko 12 a Isiraeli ngati cholowa chawo ndipo zigawo ziwiri zidzakhale za mbadwa za Yosefe.+