Ezekieli 47:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mudzatenge dzikoli kuti likhale cholowa chanu ndipo aliyense adzalandire gawo lofanana ndi la mnzake. Ine ndinalumbira kuti ndidzapereka dziko limeneli kwa makolo anu+ ndipo tsopano ndikulipereka kwa inu kuti likhale cholowa chanu.
14 Mudzatenge dzikoli kuti likhale cholowa chanu ndipo aliyense adzalandire gawo lofanana ndi la mnzake. Ine ndinalumbira kuti ndidzapereka dziko limeneli kwa makolo anu+ ndipo tsopano ndikulipereka kwa inu kuti likhale cholowa chanu.