Ezekieli 47:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbali yakumadzulo malire anu ndi Nyanja Yaikulu, kuchokera mʼmalire a mbali yakumʼmwera mpaka kukafika malo amene ayangʼanizana ndi Lebo-hamati.*+ Amenewa ndi malire akumadzulo.
20 Kumbali yakumadzulo malire anu ndi Nyanja Yaikulu, kuchokera mʼmalire a mbali yakumʼmwera mpaka kukafika malo amene ayangʼanizana ndi Lebo-hamati.*+ Amenewa ndi malire akumadzulo.