Ezekieli 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Gawo la fuko la Aseri+ lichite malire ndi gawo la fuko la Dani, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
2 Gawo la fuko la Aseri+ lichite malire ndi gawo la fuko la Dani, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.