Ezekieli 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Gawo la fuko la Nafitali+ lichite malire ndi gawo la fuko la Aseri, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
3 Gawo la fuko la Nafitali+ lichite malire ndi gawo la fuko la Aseri, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.