-
Ezekieli 48:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ansembewo akhale ndi gawo lawo kuchokera pa gawo limene mwapereka kuti likhale gawo lopatulika koposa, ndipo lichite malire ndi gawo la Alevi.
-