-
Ezekieli 48:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Alevi akhale ndi gawo pafupi ndi gawo la ansembe. Mulitali mwake likhale mikono 25,000 ndipo mulifupi likhale mikono 10,000. (Malo onsewo akhale aatali mikono 25,000 ndipo mulifupi mwake akhale okwana mikono 10,000.)
-