-
Ezekieli 48:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Miyezo ya mzindawo ndi iyi: Mbali yakumpoto ikhale mikono 4,500. Mbali yakumʼmwera ikhale mikono 4,500. Mbali yakumʼmawa ikhale mikono 4,500, ndipo mbali yakumadzulo ikhalenso mikono 4,500.
-