-
Ezekieli 48:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Malo odyetserako ziweto a mzindawo akhale mikono 250 mbali yakumpoto, mikono 250 mbali yakumʼmwera, mikono 250 mbali yakumʼmawa komanso mikono 250 mbali yakumadzulo.
-