Ezekieli 48:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu ochokera mʼmafuko onse a Isiraeli amene akugwira ntchito mumzinda ndi omwe azidzalima malo amenewa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:19 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 18
19 Anthu ochokera mʼmafuko onse a Isiraeli amene akugwira ntchito mumzinda ndi omwe azidzalima malo amenewa.+