Ezekieli 48:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Malo a Alevi komanso malo a mzinda akhale pakati pa malo a mtsogoleri. Malo a mtsogoleriwo achite malire ndi gawo la fuko la Yuda+ komanso gawo la fuko la Benjamini.
22 Malo a Alevi komanso malo a mzinda akhale pakati pa malo a mtsogoleri. Malo a mtsogoleriwo achite malire ndi gawo la fuko la Yuda+ komanso gawo la fuko la Benjamini.