Ezekieli 48:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Gawo la fuko la Simiyoni lichite malire ndi gawo la fuko la Benjamini,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
24 Gawo la fuko la Simiyoni lichite malire ndi gawo la fuko la Benjamini,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.