Ezekieli 48:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gawo la fuko la Isakara+ lichite malire ndi gawo la fuko la Simiyoni, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
25 Gawo la fuko la Isakara+ lichite malire ndi gawo la fuko la Simiyoni, kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.