Ezekieli 48:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Gawo la fuko la Zebuloni lichite malire ndi gawo la fuko la Isakara,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.+
26 Gawo la fuko la Zebuloni lichite malire ndi gawo la fuko la Isakara,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.+