Ezekieli 48:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Gawo la fuko la Gadi lichite malire ndi gawo la fuko la Zebuloni,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
27 Gawo la fuko la Gadi lichite malire ndi gawo la fuko la Zebuloni,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.