Ezekieli 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Limeneli ndi dziko lomwe mukuyenera kugawa kwa mafuko onse a Isiraeli kuti likhale cholowa chawo+ ndipo magawo awo akhale amenewa,”+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
29 Limeneli ndi dziko lomwe mukuyenera kugawa kwa mafuko onse a Isiraeli kuti likhale cholowa chawo+ ndipo magawo awo akhale amenewa,”+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.