-
Ezekieli 48:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Mayina a mageti a mzindawo akhale ofanana ndi mayina a mafuko a Isiraeli. Mbali yakumpoto kukhale mageti atatu. Geti limodzi likhale ndi dzina lakuti Rubeni, geti lina Yuda ndipo lina Levi.
-