-
Ezekieli 48:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Kumbali yakumadzulo mzindawo ukhale mikono 4,500 ndipo kukhale mageti awa: Geti limodzi likhale ndi dzina lakuti Gadi, geti lina Aseri ndipo geti lina Nafitali.
-