-
Danieli 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma Danieli anatsimikiza mumtima mwake kuti sadzidetsa ndi zakudya zabwino za mfumu kapena ndi vinyo amene ankamwa. Choncho iye anapempha mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti amulole kuti asadzidetse ndi zinthu zimenezi.
-