-
Danieli 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumuyo anauza Danieli kuti: “Ine ndikuopa mbuye wanga mfumu, amene walamula kuti muzipatsidwa chakudya ndi zakumwa zimenezi. Ndiye mukuona kuti zitha bwanji akakuonani kuti ndinu owonda kuposa anyamata* ena a msinkhu wanu? Mupangitsa kuti ndikhale* ndi mlandu pamaso pa mfumu.”
-