Danieli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako mudzayerekeze mmene ifeyo tikuonekera ndi mmene anyamata* amene akudya zakudya zabwino za mfumu akuonekera, ndipo mudzachitire atumiki anufe mogwirizana ndi zimene mudzaone.” Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, tsa. 16
13 Kenako mudzayerekeze mmene ifeyo tikuonekera ndi mmene anyamata* amene akudya zakudya zabwino za mfumu akuonekera, ndipo mudzachitire atumiki anufe mogwirizana ndi zimene mudzaone.”