Danieli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku 10 amenewo atatha, iwo ankaoneka bwino kwambiri ndipo anali athanzi* kuposa anyamata* onse amene ankadya zakudya zabwino za mfumu. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 40-41
15 Masiku 10 amenewo atatha, iwo ankaoneka bwino kwambiri ndipo anali athanzi* kuposa anyamata* onse amene ankadya zakudya zabwino za mfumu.