-
Danieli 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho, amene ankawayangʼanira uja anapitirizabe kuwapatsa zakudya zamasamba mʼmalo mwa zakudya zabwino za mfumu ndi vinyo wake.
-