Danieli 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Masiku amene mfumu inanena kuti adzabweretse anyamata aja pamaso pake atakwana,+ mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu uja anabweretsa anyamatawo pamaso pa Nebukadinezara. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Ulosi wa Danieli, tsa. 42
18 Masiku amene mfumu inanena kuti adzabweretse anyamata aja pamaso pake atakwana,+ mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu uja anabweretsa anyamatawo pamaso pa Nebukadinezara.