-
Danieli 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno mfumuyo inanena kuti: “Ine ndikudziwa kuti mukuzengereza dala kuti mukhale ndi nthawi yambiri yoganiza chifukwa mukudziwa kale zimene ndalamula.
-