-
Danieli 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Lamulo limenelo litaperekedwa ndipo amuna anzeru atatsala pangʼono kuphedwa, anthu anayambanso kufunafuna Danieli ndi anzake kuti awaphe.
-