Danieli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu nʼkuiuza kuti: “Ndapeza munthu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”
25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu nʼkuiuza kuti: “Ndapeza munthu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”