Danieli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Palibe amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga kapena anthu okhulupirira nyenyezi amene angakwanitse kukuuzani inu mfumu chinsinsi chimene mukufuna kudziwa.+
27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Palibe amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga kapena anthu okhulupirira nyenyezi amene angakwanitse kukuuzani inu mfumu chinsinsi chimene mukufuna kudziwa.+