-
Danieli 2:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Inu mfumu, mutagona pabedi lanu munayamba kuganiza za zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo ndipo Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi wakudziwitsani zimene zidzachitike.
-