-
Danieli 2:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Inuyo mfumu munalota mukuona chifaniziro chachikulu kwambiri. Chifanizirocho chinali chitaima patsogolo panu ndipo chinali chachikulu komanso chowala kwambiri ndipo chimaoneka mochititsa mantha.
-