-
Danieli 2:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Mogwirizana ndi zimene munaona kuti mapazi ndi zala zakumiyendo zinali zadongo la woumba mbiya losakanikirana ndi chitsulo, ufumuwo udzakhala wogawanika. Koma udzakhala wolimba pa zinthu zina ngati chitsulo, ngati mmene munaonera kuti chitsulocho chinali chosakanikirana ndi dongo lofewa.
-