Danieli 2:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako mfumu inamukweza pa udindo Danieli ndipo inamupatsa mphatso zambiri zabwino. Inamuikanso kuti akhale wolamulira wa chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso mkulu wa akuluakulu a boma amene ankayangʼanira amuna onse anzeru a mʼBabulo.
48 Kenako mfumu inamukweza pa udindo Danieli ndipo inamupatsa mphatso zambiri zabwino. Inamuikanso kuti akhale wolamulira wa chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso mkulu wa akuluakulu a boma amene ankayangʼanira amuna onse anzeru a mʼBabulo.