-
Danieli 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mtengowo unakula ndipo unakhala wamphamvu kwambiri. Nsonga yake inafika kumwamba ndipo umaonekera mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.
-