Danieli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho amuna amenewa anati: “Danieliyu sitimupezera chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Ulosi wa Danieli, tsa. 125
5 Choncho amuna amenewa anati: “Danieliyu sitimupezera chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+