-
Danieli 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pa nthawi imeneyo, amuna amenewa analowa mʼnyumbamo ali chigulu ndipo anapeza Danieli akuchonderera ndi kupempha Mulungu wake kuti amukomere mtima.
-