Danieli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anabweretsa mwala nʼkutseka pakhomo la* dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.
17 Ndiyeno anabweretsa mwala nʼkutseka pakhomo la* dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.