-
Danieli 6:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno kutangoyamba kuwala mʼbandakucha, mfumuyo inadzuka ndipo inapita mofulumira kudzenje la mikango lija.
-