Danieli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Mʼmasomphenya usiku, ndinaona mphepo 4 zakumwamba zikuvundula nyanja yaikulu.+