Danieli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinaonanso chilombo china chachiwiri, chooneka ngati chimbalangondo.+ Chinali chotukuka mbali imodzi ndipo mʼkamwa mwake munali nthiti zitatu pakati pa mano ake. Chilombochi chinauzidwa kuti, ‘Nyamuka, idya nyama yambiri.’+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Galamukani!,2/2011, tsa. 17 Ulosi wa Danieli, ptsa. 132-134 Nsanja ya Olonda,10/1/1986, tsa. 7
5 Ndinaonanso chilombo china chachiwiri, chooneka ngati chimbalangondo.+ Chinali chotukuka mbali imodzi ndipo mʼkamwa mwake munali nthiti zitatu pakati pa mano ake. Chilombochi chinauzidwa kuti, ‘Nyamuka, idya nyama yambiri.’+